-
Machitidwe 7:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Mose ankaganiza kuti abale akewo azindikira kuti Mulungu akuwapulumutsa pogwiritsa ntchito dzanja lake, koma iwo sanaizindikire mfundo imeneyi.
-