-
Machitidwe 7:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Tsiku lotsatira iye anapitanso kukawaona ndipo anapeza Aisiraeli ena akumenyana. Mose anayesa kuwathandiza kuti agwirizane ponena kuti, ‘Anthu inu, ndinu pachibale. Nʼchifukwa chiyani mukumenyana chonchi?’
-