Machitidwe 7:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Atamva zimenezi, Mose anathawa nʼkukakhala mʼdziko la Midiyani. Kumeneko anabereka ana aamuna awiri.+
29 Atamva zimenezi, Mose anathawa nʼkukakhala mʼdziko la Midiyani. Kumeneko anabereka ana aamuna awiri.+