Machitidwe 7:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Patapita zaka 40, mngelo anaonekera kwa iye mʼchipululu paphiri la Sinai, pachitsamba chaminga chimene chinkayaka moto.+
30 Patapita zaka 40, mngelo anaonekera kwa iye mʼchipululu paphiri la Sinai, pachitsamba chaminga chimene chinkayaka moto.+