Machitidwe 7:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Mose ataona zimenezi, anadabwa kwambiri. Koma pamene ankayandikira kuti aonetsetse, anamva mawu a Yehova* akuti,
31 Mose ataona zimenezi, anadabwa kwambiri. Koma pamene ankayandikira kuti aonetsetse, anamva mawu a Yehova* akuti,