Machitidwe 7:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Yehova* anamuuza kuti, ‘Vula nsapato zako, chifukwa malo waimawo ndi malo oyera.