Machitidwe 7:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ine ndaona kuti anthu anga omwe ali ku Iguputo akuzunzidwa kwambiri. Ndamva kubuula kwawo+ ndipo ndabwera kudzawapulumutsa. Ndiye ndikufuna ndikutume ku Iguputo.’
34 Ine ndaona kuti anthu anga omwe ali ku Iguputo akuzunzidwa kwambiri. Ndamva kubuula kwawo+ ndipo ndabwera kudzawapulumutsa. Ndiye ndikufuna ndikutume ku Iguputo.’