Machitidwe 7:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Koma makolo athu anakana kumumvera. Mʼmalomwake, anamukankhira kumbali+ ndipo mumtima mwawo anabwerera ku Iguputo.+
39 Koma makolo athu anakana kumumvera. Mʼmalomwake, anamukankhira kumbali+ ndipo mumtima mwawo anabwerera ku Iguputo.+