Machitidwe 7:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Anauza Aroni kuti, ‘Tipangire milungu kuti ititsogolere chifukwa sitikudziwa zimene zachitikira Mose, amene ankatitsogolera pochoka ku Iguputo.’+
40 Anauza Aroni kuti, ‘Tipangire milungu kuti ititsogolere chifukwa sitikudziwa zimene zachitikira Mose, amene ankatitsogolera pochoka ku Iguputo.’+