Machitidwe 7:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Choncho iwo anapanga fano la mwana wa ngʼombe mʼmasiku amenewo. Atatero anabweretsa nsembe zopereka kwa fanolo ndipo anasangalala ndi ntchito ya manja awo.+
41 Choncho iwo anapanga fano la mwana wa ngʼombe mʼmasiku amenewo. Atatero anabweretsa nsembe zopereka kwa fanolo ndipo anasangalala ndi ntchito ya manja awo.+