Machitidwe 7:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Makolo athuwo anali ndi chihema cha umboni mʼchipululu. Anachipanga potsatira malangizo amene Mulungu anapereka kwa Mose mogwirizana ndi chithunzi chimene Moseyo anachiona.+
44 Makolo athuwo anali ndi chihema cha umboni mʼchipululu. Anachipanga potsatira malangizo amene Mulungu anapereka kwa Mose mogwirizana ndi chithunzi chimene Moseyo anachiona.+