Machitidwe 7:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Mulungu anakomera mtima Davide ndipo iye anapempha mwayi woti amange nyumba yoti Mulungu wa Yakobo azikhalamo.+
46 Mulungu anakomera mtima Davide ndipo iye anapempha mwayi woti amange nyumba yoti Mulungu wa Yakobo azikhalamo.+