Machitidwe 7:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 ‘Yehova* wanena kuti, Kumwamba ndi mpando wanga wachifumu+ ndipo dziko lapansi ndi chopondapo mapazi anga.+ Ndiye kodi mungandimangire nyumba yotani? Ndipo malo oti ine ndingapumulirepo ali kuti? Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:49 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 49
49 ‘Yehova* wanena kuti, Kumwamba ndi mpando wanga wachifumu+ ndipo dziko lapansi ndi chopondapo mapazi anga.+ Ndiye kodi mungandimangire nyumba yotani? Ndipo malo oti ine ndingapumulirepo ali kuti?