Machitidwe 7:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Anthu okanika inu ndiponso osachita mdulidwe wamumtima ndi mʼmakutu. Nthawi zonse mumatsutsana ndi mzimu woyera. Mukuchita zinthu ngati mmene ankachitira makolo anu.+
51 Anthu okanika inu ndiponso osachita mdulidwe wamumtima ndi mʼmakutu. Nthawi zonse mumatsutsana ndi mzimu woyera. Mukuchita zinthu ngati mmene ankachitira makolo anu.+