Machitidwe 7:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Ndi mneneri uti amene makolo anuwo sanamuzunze?+ Iwo anapha anthu amene analengezeratu za kubwera kwa wolungamayo,+ amene inuyo munamupereka ndiponso kumupha.+
52 Ndi mneneri uti amene makolo anuwo sanamuzunze?+ Iwo anapha anthu amene analengezeratu za kubwera kwa wolungamayo,+ amene inuyo munamupereka ndiponso kumupha.+