Machitidwe 7:60 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 60 Kenako anagwada nʼkufuula ndi mawu amphamvu kuti: “Yehova,* musawaimbe mlandu wa tchimo ili.”+ Atanena zimenezi anafa.*
60 Kenako anagwada nʼkufuula ndi mawu amphamvu kuti: “Yehova,* musawaimbe mlandu wa tchimo ili.”+ Atanena zimenezi anafa.*