Machitidwe 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Saulo anavomereza zoti Sitefano aphedwe.+ Tsiku limenelo, mpingo umene unali ku Yerusalemu unayamba kuzunzidwa koopsa. Choncho ophunzira onse, kupatula atumwi okha, anabalalika nʼkupita mʼzigawo za Yudeya ndi Samariya.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:1 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),1/2020, tsa. 18 Nsanja ya Olonda,5/15/2008, ptsa. 22-2310/15/2007, tsa. 226/15/1999, ptsa. 29-30
8 Saulo anavomereza zoti Sitefano aphedwe.+ Tsiku limenelo, mpingo umene unali ku Yerusalemu unayamba kuzunzidwa koopsa. Choncho ophunzira onse, kupatula atumwi okha, anabalalika nʼkupita mʼzigawo za Yudeya ndi Samariya.+
8:1 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),1/2020, tsa. 18 Nsanja ya Olonda,5/15/2008, ptsa. 22-2310/15/2007, tsa. 226/15/1999, ptsa. 29-30