Machitidwe 8:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Koma mngelo wa Yehova*+ analankhula kwa Filipo kuti: “Nyamuka ndipo upite kumʼmwera, kumsewu wochokera ku Yerusalemu kupita ku Gaza.” (Umenewu ndi msewu wa mʼchipululu.)
26 Koma mngelo wa Yehova*+ analankhula kwa Filipo kuti: “Nyamuka ndipo upite kumʼmwera, kumsewu wochokera ku Yerusalemu kupita ku Gaza.” (Umenewu ndi msewu wa mʼchipululu.)