-
Machitidwe 8:30Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
30 Filipo anathamanga nʼkumayenda mʼmbali mwa galetalo ndipo anamumva akuwerenga mokweza ulosi wa mneneri Yesaya. Filipo anamufunsa kuti: “Kodi mukumvetsa zimene mukuwerengazo?”
-