-
Machitidwe 8:38Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
38 Atatero analamula kuti galetalo liime. Kenako Filipo ndi nduna ija anatsika nʼkulowa mʼmadzimo, ndipo Filipo anabatiza ndunayo.
-