-
Machitidwe 9:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Kenako Saulo anaimirira, koma ngakhale kuti ankayangʼana, sankaona chilichonse. Choncho anamugwira dzanja nʼkumulondolera ku Damasiko.
-