Machitidwe 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ku Damasiko kunali wophunzira wina dzina lake Hananiya.+ Ndiyeno Ambuye analankhula naye mʼmasomphenya kuti: “Hananiya!” Iye anayankha kuti: “Ine Ambuye.”
10 Ku Damasiko kunali wophunzira wina dzina lake Hananiya.+ Ndiyeno Ambuye analankhula naye mʼmasomphenya kuti: “Hananiya!” Iye anayankha kuti: “Ine Ambuye.”