-
Machitidwe 9:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Nthawi yomweyo tinthu tooneka ngati mamba a nsomba tinagwa kuchokera mʼmaso mwa Saulo ndipo anayambanso kuona. Kenako anapita kukabatizidwa.
-