Machitidwe 9:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Atafika ku Yerusalemu+ anayesetsa kuti agwirizane ndi ophunzira kumeneko. Koma onse ankamuopa, chifukwa sankakhulupirira kuti ndi wophunzira. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:26 Nsanja ya Olonda,4/15/1998, tsa. 21
26 Atafika ku Yerusalemu+ anayesetsa kuti agwirizane ndi ophunzira kumeneko. Koma onse ankamuopa, chifukwa sankakhulupirira kuti ndi wophunzira.