-
Machitidwe 9:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Zitatero anapitiriza kukhala nawo nʼkumayenda momasuka mu Yerusalemu, ndipo ankalankhula molimba mtima mʼdzina la Ambuye.
-