Machitidwe 9:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Ku Yopa kunali wophunzira wina dzina lake Tabita, dzina limene limamasuliridwa kuti Dorika.* Tabita ankachita zinthu zambiri zabwino ndiponso ankapatsa ena mphatso zambiri zachifundo. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:36 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 67 Nsanja ya Olonda,9/1/1989, tsa. 17
36 Ku Yopa kunali wophunzira wina dzina lake Tabita, dzina limene limamasuliridwa kuti Dorika.* Tabita ankachita zinthu zambiri zabwino ndiponso ankapatsa ena mphatso zambiri zachifundo.