-
Machitidwe 9:37Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
37 Ndiyeno mʼmasiku amenewo iye anadwala ndipo anamwalira. Choncho anamusambitsa nʼkukamugoneka mʼchipinda chamʼmwamba.
-