Machitidwe 10:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndiyeno Koneliyo anati: “Masiku 4 apitawo, ine ndikupemphera mʼnyumba mwanga muno cha mʼma 3 koloko masana,* ndinangoona munthu wovala zowala ataima kutsogolo kwanga.
30 Ndiyeno Koneliyo anati: “Masiku 4 apitawo, ine ndikupemphera mʼnyumba mwanga muno cha mʼma 3 koloko masana,* ndinangoona munthu wovala zowala ataima kutsogolo kwanga.