Machitidwe 10:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Aneneri onse amachitira umboni za iyeyu,+ kuti aliyense womukhulupirira, machimo ake amakhululukidwa mʼdzina lake.”+
43 Aneneri onse amachitira umboni za iyeyu,+ kuti aliyense womukhulupirira, machimo ake amakhululukidwa mʼdzina lake.”+