Machitidwe 10:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Atatero anawalamula kuti abatizidwe mʼdzina la Yesu Khristu.+ Ndiyeno iwo anamupempha kuti akhalebe nawo kwa masiku angapo.
48 Atatero anawalamula kuti abatizidwe mʼdzina la Yesu Khristu.+ Ndiyeno iwo anamupempha kuti akhalebe nawo kwa masiku angapo.