Machitidwe 11:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Ine ndikupemphera mumzinda wa Yopa, ndinaona masomphenya. Ndinaona chinthu chooneka ngati chinsalu chachikulu chikutsika kuchokera kumwamba. Chinthucho anachigwira mʼmakona onse 4 nʼkuchitsitsira pamene ndinali.+
5 “Ine ndikupemphera mumzinda wa Yopa, ndinaona masomphenya. Ndinaona chinthu chooneka ngati chinsalu chachikulu chikutsika kuchokera kumwamba. Chinthucho anachigwira mʼmakona onse 4 nʼkuchitsitsira pamene ndinali.+