-
Machitidwe 11:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Nditachiyangʼanitsitsa, ndinaonamo nyama za miyendo 4 zapadziko lapansi, nyama zakutchire, nyama zokwawa komanso mbalame zamumlengalenga.
-