-
Machitidwe 11:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Kenako mzimu unandiuza kuti ndipite nawo, ndisakayikire ngakhale pangʼono. Abale 6 awa anapita nane limodzi ndipo tinakalowa mʼnyumba ya munthuyo.
-