Machitidwe 11:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Zitatero ndinakumbukira mawu amene Ambuye ankakonda kunena aja akuti, ‘Yohane ankabatiza ndi madzi,+ koma inu mudzabatizidwa ndi mzimu woyera.’+
16 Zitatero ndinakumbukira mawu amene Ambuye ankakonda kunena aja akuti, ‘Yohane ankabatiza ndi madzi,+ koma inu mudzabatizidwa ndi mzimu woyera.’+