Machitidwe 11:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho ngati Mulungu anawapatsa mphatso yaulere yomwenso anatipatsa ifeyo amene tinakhulupirira mwa Ambuye Yesu Khristu, ndine ndani kuti ndiletse Mulungu?”+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:17 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 73
17 Choncho ngati Mulungu anawapatsa mphatso yaulere yomwenso anatipatsa ifeyo amene tinakhulupirira mwa Ambuye Yesu Khristu, ndine ndani kuti ndiletse Mulungu?”+