Machitidwe 11:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Atamva zimenezi, anasiya kumutsutsa,* ndipo anatamanda Mulungu kuti: “Ndiye kuti Mulungu waperekanso mwayi kwa anthu a mitundu ina kuti nawonso alape nʼkudzapeza moyo.”+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:18 Nsanja ya Olonda,7/15/1996, tsa. 16
18 Atamva zimenezi, anasiya kumutsutsa,* ndipo anatamanda Mulungu kuti: “Ndiye kuti Mulungu waperekanso mwayi kwa anthu a mitundu ina kuti nawonso alape nʼkudzapeza moyo.”+