-
Machitidwe 11:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Koma ena mwa anthuwa anali a ku Kupuro ndi ku Kurene. Iwowa atafika ku Antiokeya anayamba kulengeza uthenga wabwino wa Ambuye Yesu kwa anthu olankhula Chigiriki.
-