Machitidwe 11:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Dzanja la Yehova* linkawathandiza ndipo anthu ambiri anakhulupirira nʼkuyamba kutsatira Ambuye.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:21 Nsanja ya Olonda,1/1/1989, ptsa. 11-12