Machitidwe 11:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mpingo wa ku Yerusalemu unamva za anthuwa ndipo unatumiza Baranaba+ kuti apite ku Antiokeya. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:22 Nsanja ya Olonda,7/15/2000, tsa. 25