Machitidwe 11:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Baranaba anali munthu wabwino komanso wa chikhulupiriro cholimba. Iye ankatsogoleredwa kwambiri ndi mzimu woyera ndipo anthu enanso ambiri anakhulupirira Ambuye.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:24 Nsanja ya Olonda,7/15/2000, tsa. 25
24 Baranaba anali munthu wabwino komanso wa chikhulupiriro cholimba. Iye ankatsogoleredwa kwambiri ndi mzimu woyera ndipo anthu enanso ambiri anakhulupirira Ambuye.+