-
Machitidwe 12:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Iye anatuluka nʼkumamutsatira, koma sanadziwe kuti zimene zinkachitika ndi mngelozo zinalidi zenizeni. Ankangoganiza kuti akuona masomphenya.
-