Machitidwe 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma Petulo atayamba kuzindikira zimene zikuchitika anati: “Tsopano ndadziwa kuti Yehova* ndi amene watumiza mngelo wake kudzandipulumutsa mʼmanja mwa Herode komanso ku zinthu zonse zimene Ayuda amayembekezera kuti zichitike.”+
11 Koma Petulo atayamba kuzindikira zimene zikuchitika anati: “Tsopano ndadziwa kuti Yehova* ndi amene watumiza mngelo wake kudzandipulumutsa mʼmanja mwa Herode komanso ku zinthu zonse zimene Ayuda amayembekezera kuti zichitike.”+