Machitidwe 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Atazindikira zimenezi, iye anapita kunyumba kwa Mariya, mayi ake a Yohane wotchedwanso Maliko.+ Kumeneko anthu ambiri anali atasonkhana nʼkumapemphera. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:12 Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 18, 80, 118 Nsanja ya Olonda,3/15/2010, ptsa. 6-72/1/2008, tsa. 243/1/2000, tsa. 16
12 Atazindikira zimenezi, iye anapita kunyumba kwa Mariya, mayi ake a Yohane wotchedwanso Maliko.+ Kumeneko anthu ambiri anali atasonkhana nʼkumapemphera.
12:12 Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 18, 80, 118 Nsanja ya Olonda,3/15/2010, ptsa. 6-72/1/2008, tsa. 243/1/2000, tsa. 16