Machitidwe 12:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma iye anawauza ndi manja kuti akhale chete, ndipo anawafotokozera mwatsatanetsatane mmene Yehova* anamutulutsira mʼndende. Kenako anati: “Nkhani imeneyi mukauze Yakobo+ ndi abale.” Atatero anatuluka nʼkupita kwina. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:17 Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 81, 112 Nsanja ya Olonda,5/15/1997, tsa. 166/1/1990, tsa. 20
17 Koma iye anawauza ndi manja kuti akhale chete, ndipo anawafotokozera mwatsatanetsatane mmene Yehova* anamutulutsira mʼndende. Kenako anati: “Nkhani imeneyi mukauze Yakobo+ ndi abale.” Atatero anatuluka nʼkupita kwina.