Machitidwe 13:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mumpingo wa ku Antiokeya munali aneneri ndi aphunzitsi.+ Iwo anali Baranaba, Sumiyoni wotchedwa Nigeri, Lukiyo wa ku Kurene, Saulo ndiponso Manayeni amene anaphunzira pamodzi ndi Herode wolamulira chigawo. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:1 Nsanja ya Olonda,6/15/1990, tsa. 10
13 Mumpingo wa ku Antiokeya munali aneneri ndi aphunzitsi.+ Iwo anali Baranaba, Sumiyoni wotchedwa Nigeri, Lukiyo wa ku Kurene, Saulo ndiponso Manayeni amene anaphunzira pamodzi ndi Herode wolamulira chigawo.