Machitidwe 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Atamaliza kusala kudya ndiponso kupemphera, anawagwira pamutu* nʼkuwalola kuti apite. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:3 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 86