-
Machitidwe 13:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Choncho anthu amenewa, omwe anatumizidwa ndi mzimu woyera, anapita ku Selukeya ndipo kuchokera kumeneko anayenda ulendo wapamadzi kupita ku Kupuro.
-