-
Machitidwe 13:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Iwo anayenda pachilumba chonse cha Kupuro mpaka kukafika ku Pafo. Kumeneko anakumana ndi Myuda wina wamatsenga dzina lake Bara-Yesu, yemwe analinso mneneri wabodza.
-