-
Machitidwe 13:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Iyeyu anali limodzi ndi bwanamkubwa Serigio Paulo, yemwe anali munthu wanzeru. Bwanamkubwayu anaitana Baranaba ndi Saulo, chifukwa ankafunitsitsa kumva mawu a Mulungu.
-