-
Machitidwe 13:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Koma Elima, wamatsenga, (chifukwa dzina lakeli amalimasulira chonchi) anayamba kutsutsana nawo. Iye ankayesetsa kuti bwanamkubwayo asakhulupirire Ambuye.
-